Marko 1:3 - Buku Lopatulika Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Liwu la munthu wofuula m'chipululu: akunena kuti, ‘Konzani mseu wodzadzeramo Ambuye, ongolani njira zoti adzapitemo.’ ” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Mawu a wofuwula mʼchipululu, ‘Konzani njira ya Ambuye, wongolani njira zake.’ ” |
Pakuti uyu ndiye ananenayo Yesaya mneneri, kuti, Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake.
pa ukulu wansembe wao wa Anasi ndi Kayafa, panadza mau a Mulungu kwa Yohane mwana wa Zekariya m'chipululu.
Yohane achita umboni za Iye, nafuula nati, Uyu ndiye amene ndinanena za Iye, Wakudzayo pambuyo panga analipo ndisanabadwe ine; chifukwa anakhala woyamba wa ine.