Tsiku lomwelo Yehova anapangana chipangano ndi Abramu, nati, Ndidzapatsa mbeu zako dziko ili, kuyambira pamtsinje wa ku Ejipito kufikira pamtsinje waukulu, mtsinje wa Yufurate:
Genesis 9:8 - Buku Lopatulika Ndipo Mulungu ananena kwa Nowa ndi kwa ana ake pamodzi naye, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mulungu ananena kwa Nowa ndi kwa ana ake pamodzi naye, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mulungu adauza Nowa ndi ana ake kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mulungu anawuza Nowa ndi ana ake kuti, |
Tsiku lomwelo Yehova anapangana chipangano ndi Abramu, nati, Ndidzapatsa mbeu zako dziko ili, kuyambira pamtsinje wa ku Ejipito kufikira pamtsinje waukulu, mtsinje wa Yufurate:
Ndipo Ine, taonani, Ine ndikhazikitsa pangano langa pamodzi ndi inu, ndi mbeu zanu pambuyo panu;