Genesis 10:13 - Buku Lopatulika Ejipito ndipo anabala Ludimu, ndi Anamimu, ndi Lehabu, ndi Nafituhimu, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ejipito ndipo anabala Ludimu, ndi Anamimu, ndi Lehabu, ndi Nafituhimu, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ejipito ndi amene anali kholo la anthu a ku Ludi, Anamu, Lehabu, Nafutu, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Igupto ndiye kholo la Aludi, Aanami, Alehabu, Anafutu, |
Kwerani, inu akavalo; chitani misala, inu magaleta, atuluke amphamvu; Akusi ndi Aputi, ogwira chikopa; ndi Aludi, amene agwira ndi kukoka uta.
Kusi, ndi Puti, ndi Ludi, ndi osokonezeka onse, ndi Libiya, ndi anthu a dziko lopangana nao, adzagwa pamodzi nao ndi lupanga.