Ine ndidzakhala chikole, pa manja anga mudzamfunsa: ndikapanda kumbwezera kwa inu ndi kumuimitsa pamaso panu, chifukwa chake chidzakhala pa ine masiku onse:
Filemoni 1:18 - Buku Lopatulika Koma ngati anakulakwira kanthu, kapena wokongola kanthu, kanthu, kapena wakongola kanthu, undiwerengere ine kameneko; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma ngati anakulakwira kanthu, kapena wokongola kanthu, kanthu, kapena wakongola kanthu, undiwerengere ine kameneko; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ngati adakulakwirapo, kapena ali ndi ngongole kwa iwe, ngongoleyo ikhale yanga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ngati anakulakwira kapena kukongola kanthu kalikonse, ndidzalipira ineyo. |
Ine ndidzakhala chikole, pa manja anga mudzamfunsa: ndikapanda kumbwezera kwa inu ndi kumuimitsa pamaso panu, chifukwa chake chidzakhala pa ine masiku onse:
ine Paulo ndichilemba ndi dzanja langa, ndidzachibwezera ine; kuti ndisanene nawe kuti iwe ndiwe mangawa anga.