Awa ndi omwewo ananena ndi Farao, mfumu ya Aejipito, awatulutse ana a Israele mu Ejipito; Mose ndi Aroni amenewa.
Eksodo 6:28 - Buku Lopatulika Ndipo kunali, tsiku limene Yehova ananena ndi Mose m'dziko la Ejipito, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo kunali, tsiku limene Yehova ananena ndi Mose m'dziko la Ejipito, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene Chauta adalankhula ndi Mose ku dziko la Ejipito, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsopano pamene Yehova anayankhula kwa Mose mu Igupto, |
Awa ndi omwewo ananena ndi Farao, mfumu ya Aejipito, awatulutse ana a Israele mu Ejipito; Mose ndi Aroni amenewa.
Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, Ine ndine Yehova; lankhula ndi Farao mfumu ya Aejipito zonsezi Ine ndizinena nawe.