Ndipo Aroni azifukizapo chofukiza cha zonunkhira zokoma m'mawa ndi m'mawa, pamene akonza nyalizo, achifukize.
Eksodo 40:27 - Buku Lopatulika nafukizapo chofukiza cha fungo lokoma; monga Yehova adamuuza Mose. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 nafukizapo chofukiza cha fungo lokoma; monga Yehova adamuuza Mose. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adafukiza lubani wa fungo lokoma paguwapo, monga momwe Chauta adamlamulira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo anapserezapo lubani wonunkhira monga Yehova anamulamulira. |
Ndipo Aroni azifukizapo chofukiza cha zonunkhira zokoma m'mawa ndi m'mawa, pamene akonza nyalizo, achifukize.