Ndi mzere wachitatu wa lesemu, sibu, ndi akalama.
Pa mzere wachitatu adaika miyala ya opela, agate ndi ametisiti,
mzere wachitatu anayikapo miyala ya opera, agate ndi ametisiti;
ndi mzere wachitatu wa lesemu, sibu, ndi akalama;
Ndi mzere wachiwiri wa nofeki, safiro, ndi yahalomu.
Ndi mzere wachinai wa tarisisi, sohamu, ndi yasefe; inakhala yogwirika ndi golide maikidwe ake.