Eksodo 39:13 - Buku Lopatulika13 Ndi mzere wachinai wa tarisisi, sohamu, ndi yasefe; inakhala yogwirika ndi golide maikidwe ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndi mzere wachinai wa tarisisi, sohamu, ndi yasefe; inakhala yogwirika ndi golide maikidwe ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 ndipo pa mzere wachinai adaika miyala ya berili, onikisi ndi yasipara. Miyalayo adaiika m'zoikamo zagolide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 mzere wachinayi anayikapo miyala ya topazi, onikisi ndi yasipa. Miyalayi anayiyika mu zoyikamo zagolide. Onani mutuwo |
Ndi mphamvu yanga yonse tsono ndakonzeratu nyumba ya Mulungu wanga, golide wa zija zagolide ndi siliva wa zija zasiliva, ndi mkuwa wa zija zamkuwa, chitsulo cha zija zachitsulo, ndi mtengo wa zija zamtengo, miyala yaberulo, ndi miyala yoikika, miyala yokometsera, ndi ya mawangamawanga, ndi miyala ya mtengo wake ya mitundumitundu ndi miyala yansangalabwe yochuluka.