Ndipo uikepo miyala yoikikapo, mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba;
Eksodo 39:11 - Buku Lopatulika Ndi mzere wachiwiri wa nofeki, safiro, ndi yahalomu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi mzere wachiwiri wa nofeki, safiro, ndi yahalomu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pa mzere wachiŵiri adaika miyala ya emeradi, safiro ndi daimondi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero mzere wachiwiri anayikapo miyala ya emeradi, safiro ndi dayimondi; |
Ndipo uikepo miyala yoikikapo, mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba;
Ndipo anaika pomwepo mizere inai ya miyala; mzere wa odemu, pitida, ndi bareketi, ndiyo ya mzere woyamba.
Unali mu Edeni, munda wa Mulungu, mwala uliwonse wa mtengo wake unali chofunda chako, sardiyo, topazi, diamondi, berulo, sohamu, ndi yaspi, safiro, nofeki, bareketi, ndi golide; malingaka ako ndi akazi ako anakutumikira tsiku lolengedwa iwe zinakonzekeratu.