Koma ali nayo mphamvu ndani yakummangira Iye nyumba, popeza thambo lam'mwambamwamba silimfikira? Ndine yani ine tsono, kuti ndimmangire nyumba, koma kumfukizira chofukiza ndiko?
Eksodo 31:5 - Buku Lopatulika ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kozokota mtengo, kuchita ntchito zilizonse. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kozokota mtengo, kuchita ntchito zilizonse. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Akudziŵanso kuzokota miyala yogwira nayo ntchito, kujoba mitengo, ndi kuchita zaluso zonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kusema ndi kuyika miyala yokongola, kukonza zinthu zamatabwa ndiponso kugwira ntchito ina iliyonse yamanja. |
Koma ali nayo mphamvu ndani yakummangira Iye nyumba, popeza thambo lam'mwambamwamba silimfikira? Ndine yani ine tsono, kuti ndimmangire nyumba, koma kumfukizira chofukiza ndiko?
Ndipo Ine, taona, ndampatsa Oholiyabu, mwana wa Ahisamaki, wa fuko la Dani, akhale naye; ndipo ndaika luso m'mitima ya onse a mtima waluso, kuti apange zonse ndakuuza iwe;