Ndipo anadulitsa ndi matabwa amkungudza mikono makumi awiri m'kati mwa nyumba m'tsogolo mwake, kuyambira pansi kulekeza kumitanda; ichi anamanga kukhala chipinda chamkati, malo opatulika kwambiri.
Eksodo 26:23 - Buku Lopatulika Nupange matabwa awiri angodya za chihema cha kumbuyo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nupange matabwa awiri angodya za Kachisi za kumbuyo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kumbuyo kwa chihema konko, pangodya pakhale mafulemu aŵiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo upangenso maferemu awiri a pa ngodya yakumbuyo kwenikweni kwa tenti. |
Ndipo anadulitsa ndi matabwa amkungudza mikono makumi awiri m'kati mwa nyumba m'tsogolo mwake, kuyambira pansi kulekeza kumitanda; ichi anamanga kukhala chipinda chamkati, malo opatulika kwambiri.
Ndipo akhale ophatikizika pamodzi patsinde, nakhalenso ophatikizika pamodzi kumutu kwake ndi mphete imodzi; azitero onse awiri; azikhala angodya ziwiri.