Eksodo 25:3 - Buku Lopatulika Ndipo choperekacho uchilandire kwa iwo ndi ichi: golide, ndi siliva, ndi mkuwa, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo choperekacho uchilandire kwa iwo ndi ichi: golide, ndi siliva, ndi mkuwa, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Zopereka zimene ulandirezo ndi izi: golide, siliva, mkuŵa, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zopereka zimene ulandire kwa anthuwo ndi izi: Golide, siliva ndi mkuwa. |
Lankhula ndi ana a Israele, kuti anditengere chopereka; ulandire chopereka changa kwa munthu aliyense mtima wake umfunitsa mwini.
ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi ubweya wa mbuzi;
Ndipo atenge golide, ndi lamadzi ndi lofiirira ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.
dziko loti mudzadyamo mkate wosapereweza; simudzasowamo kanthu; dziko loti miyala yake nja chitsulo, ndi m'mapiri ake mukumbe mkuwa.