Chimene chinazomoledwa ndi chilombo sindinachitengere kwa iwe; ndekha ndinalipira; padzanja langa unachifuna, chingakhale chobedwa kapena pausiku kapena pausana.
Eksodo 22:12 - Buku Lopatulika Koma ngati chidabedwa kwaoko ndithu, alipe kwa mwiniyo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma ngati chidabedwa kwaoko ndithu, alipe kwa mwiniyo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma ngati choŵetacho chidabedwa, mwiniwakeyo adzalipidwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma ngati chiwetocho chinabedwa, iye ayenera kubwezera mwini wakeyo. |
Chimene chinazomoledwa ndi chilombo sindinachitengere kwa iwe; ndekha ndinalipira; padzanja langa unachifuna, chingakhale chobedwa kapena pausiku kapena pausana.
lumbiro la Yehova likhale pakati pa iwo awiri, kuti sanatulutse dzanja lake pa chuma cha mnansi wake; ndipo mwiniyo azivomereza, ndipo asalipe.
Munthu akaikiza ndalama kapena chuma kwa mnansi wake, ndipo zibedwa m'nyumba ya munthuyo; akapeza mbala, ilipe chowirikiza.