Eksodo 21:10 - Buku Lopatulika Akamtengera mkazi wina, asachepetse chakudya chake, zovala zake, ndi za ukwati zakezake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Akamtengera mkazi wina, asachepetse chakudya chake, zovala zake, ndi za ukwati zakezake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Akakwatira mkazi wina, ayenera kupitirira kumpatsa woyambayo chakudya ndi zovala. Azimlolanso zonse zomuyenera ngati mkazi wake, monga ankachitira kale. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ngati akwatira mkazi wina, asamumane woyambayo chakudya ngakhale chovala ndipo apiritirize kugona naye ngati mkazi wake. |