Eksodo 21:10 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ngati akwatira mkazi wina, asamumane woyambayo chakudya ngakhale chovala ndipo apiritirize kugona naye ngati mkazi wake. Onani mutuwoBuku Lopatulika10 Akamtengera mkazi wina, asachepetse chakudya chake, zovala zake, ndi za ukwati zakezake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Akamtengera mkazi wina, asachepetse chakudya chake, zovala zake, ndi za ukwati zakezake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Akakwatira mkazi wina, ayenera kupitirira kumpatsa woyambayo chakudya ndi zovala. Azimlolanso zonse zomuyenera ngati mkazi wake, monga ankachitira kale. Onani mutuwo |