Ndipo panali pamene Israele anakhala m'dzikomo, Rubeni anamuka nagona ndi Biliha, mkazi wamng'ono wa atate wake: ndipo Israele anamva. Ana aamuna a Yakobo anali khumi ndi awiri:
Eksodo 2:1 - Buku Lopatulika Ndipo anamuka munthu wa banja la Levi, natenga mwana wamkazi wa Levi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anamuka munthu wa banja la Levi, natenga mwana wamkazi wa Levi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Munthu wina wa fuko la Levi adakwatira mkazi wa fuko lomwelo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo munthu wina wa fuko la Levi anakwatira mkazi wa fuko lomwelo. |
Ndipo panali pamene Israele anakhala m'dzikomo, Rubeni anamuka nagona ndi Biliha, mkazi wamng'ono wa atate wake: ndipo Israele anamva. Ana aamuna a Yakobo anali khumi ndi awiri:
Hadadi uja anathawa, iyeyo ndi a ku Edomu ena, akapolo a atate wake pamodzi naye, kunka ku Ejipito, Hadadiyo akali mwana.
Ndipo dzina lake la mkazi wake wa Amuramu ndiye Yokebede, mwana wamkazi wa Levi, wobadwira Levi mu Ejipito; ndipo iye anambalira Amuramu, Aroni ndi Mose, ndi Miriyamu mlongo wao.