Ndipo Mose anavomera kukhala naye munthuyo; ndipo anampatsa Mose mwana wake wamkazi Zipora.
Eksodo 18:2 - Buku Lopatulika Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anabwera naye Zipora mkazi wa Mose (atamtuma kwao), ndi ana ake awiri; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anabwera naye Zipora mkazi wa Mose (atamtuma kwao), ndi ana ake awiri; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero adabwera ndi Zipora, mkazi wa Mose, amene Moseyo anali atamsiya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mose atamubweza Zipora, mkazi wake, Yetero, mpongozi wake anamulandira |
Ndipo Mose anavomera kukhala naye munthuyo; ndipo anampatsa Mose mwana wake wamkazi Zipora.