Eksodo 16:13 - Buku Lopatulika Ndipo kunali madzulo zinakwera zinziri, ndipo zinakuta tsasa, ndi m'mawa padagwa mame pozungulira tsasa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo kunali madzulo zinakwera zinziri, ndipo zinakuta tsasa, ndi m'mawa padagwa mame pozungulira tsasa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero madzulo kudagwa zinziri, ndipo zidadzaza ponseponse pamahemapo. M'maŵa ndithu padagwa mame ponse pozungulira mahemawo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Madzulo amenewo panatuluka zinziri zimene zinali ponseponse pa misasa yawo, ndipo mmawa panali mame kuzungulira misasa yawo. |