Ndipo panali pamene Israele anakhala m'dzikomo, Rubeni anamuka nagona ndi Biliha, mkazi wamng'ono wa atate wake: ndipo Israele anamva. Ana aamuna a Yakobo anali khumi ndi awiri:
Eksodo 1:2 - Buku Lopatulika Rubeni, Simeoni, Levi ndi Yuda; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Rubeni, Simeoni, Levi ndi Yuda; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Rubeni, Simeoni, Levi, Yuda, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Rubeni, Simeoni, Levi, Yuda; |
Ndipo panali pamene Israele anakhala m'dzikomo, Rubeni anamuka nagona ndi Biliha, mkazi wamng'ono wa atate wake: ndipo Israele anamva. Ana aamuna a Yakobo anali khumi ndi awiri:
Amenewa ndi ana a Biliha, amene Labani anampatsa Rakele mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo; anthu onse ndiwo asanu ndi awiri.
Ndipo maina a ana a Israele, amene analowa mu Ejipito ndi Yakobo ndi awa, analowa munthu ndi banja lake: