Genesis 46:25 - Buku Lopatulika25 Amenewa ndi ana a Biliha, amene Labani anampatsa Rakele mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo; anthu onse ndiwo asanu ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Amenewa ndi ana a Biliha, amene Labani anampatsa Rakele mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo; anthu onse ndiwo asanu ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 (Asanu ndi aŵiriŵa ndiwo adzukulu a Yakobe amene adabadwa mwa Biliha, amene Labani adaapereka kwa mwana wake Rakele.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Amenewa ndi zidzukulu za Yakobo mwa Biliha amene Labani anapereka kwa mwana wake Rakele. Onse pamodzi analipo asanu ndi awiri. Onani mutuwo |