Pamenepo mupenye maonekedwe athu ndi maonekedwe a anyamata akudya chakudya cha mfumu; ndi monga umo muonera, muchitire anyamata anu.
Danieli 1:14 - Buku Lopatulika Ndipo anawamvera mau awa, nawayesa masiku khumi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anawamvera mau awa, nawayesa masiku khumi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho anawavomera ndipo anawayesa pa masiku khumi. |
Pamenepo mupenye maonekedwe athu ndi maonekedwe a anyamata akudya chakudya cha mfumu; ndi monga umo muonera, muchitire anyamata anu.
Atatha masiku khumiwo tsono, anaona kuti maonekedwe ao ndi kunenepa kwao anaposa anyamata onse adadyawo zakudya za mfumu.
Usaope zimene uti udzamve kuwawa; taona, mdierekezi adzaponya ena a inu m'nyumba yandende, kuti mukayesedwe; ndipo mudzakhala nacho chisautso masiku khumi. Khala wokhulupirika kufikira imfa, ndipo ndidzakupatsa iwe korona wa moyo.