Ndipo Yowabu anatumiza ku Tekowa, natenga kumeneko mkazi wanzeru, nanena naye, Ukokomezeke monga mfedwa, nuvale zovala za pamaliro, osadzola mafuta, koma ukhale ngati munthu wamkazi wakulira akufa nthawi yaikulu.
2 Samueli 23:26 - Buku Lopatulika Helezi Mpaliti, Ira mwana wa Ikesi Mtekowa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Helezi Mpaliti, Ira mwana wa Ikesi Mtekowa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Helezi Mpeleti, Ira mwana wa Ikesi wa ku Tekowa, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Helezi Mpaliti, Ira mwana wa Ikesi wa ku Tekowa, |