Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 23:27 - Buku Lopatulika

27 Abiyezere Mwanatoti, Mebunai Muhusa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Abiyezere Mwanatoti, Mebunai Muhusa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Abiyezere wa ku Anatoti, Mebunai Muhusa,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Abiezeri wa ku Anatoti, Sibekai Mhusati,

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 23:27
5 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali chitapita ichi, kunalinso nkhondo ndi Afilisti ku Gobu; pamenepo Sibekai Muhusa anapha Safi, ndiye wa ana a Rafa.


nati, Pali Mulungu wanga, kukhale kutali kwa ine kuchita ichi. Ngati ndidzamwa mwazi wa anthu awa? Akadataya moyo wao, inde akadataya moyo wao, pakukatenga madziwa. M'mwemo sanafune kuwamwa. Izi anazichita atatu amphamvuwa.


Ira mwana wa Ikesi wa ku Tekowa, Abiyezere wa ku Anatoti,


Wachisanu ndi chinai wa mwezi wachisanu ndi chinai ndiye Abiyezere Mwanatoti wa Abenjamini; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.


Anatoti ndi mabusa ake, ndi Alimoni ndi mabusa ake; mizinda inai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa