nulimbika mumtima kuti iwe wekha uli wotsogolera wa akhungu, nyali ya amene akhala mumdima,
2 Akorinto 7:16 - Buku Lopatulika Ndikondwera kuti m'zonse ndilimbika mtima za inu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndikondwera kuti m'zonse ndilimbika mtima za inu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndikukondwa kuti ndingathe kukukhulupirirani pa zonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndine wokondwa kuti ndingathe kukukhulupirirani pa zonse. |
nulimbika mumtima kuti iwe wekha uli wotsogolera wa akhungu, nyali ya amene akhala mumdima,
Ndipo ndinalemba ichi chomwe, kuti pakudza ndisakhale nacho chisoni kwa iwo amene ayenera kukondweretsa ine; ndi kukhulupirira mwa inu nonse, kuti chimwemwe changa ndi chanu cha inu nonse.
koma tikhulupirira mwa Ambuye za inu, kuti mumachita, ndiponso mudzachita zimene tikulamulirani.
Pokhulupirira kumvera kwako ndikulembera iwe, podziwa kuti udzachitanso koposa chimene ndinena.
Momwemo, ndingakhale ndili nako kulimbika mtima kwakukulu mu Khristu kukulamulira chimene chiyenera,