Chifukwa cha ichi ndilembera izi pokhala palibe ine, kuti pokhala ndili pomwepo ndingachite mowawitsa, monga mwa ulamuliro umene Ambuye anandipatsa ine wakumangirira, ndipo si wakugwetsa.
2 Akorinto 2:6 - Buku Lopatulika Kwa wotereyo chilango ichi chidachitika ndi ambiri chikwanira; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Kwa wotereyo chilango ichi chidachitika ndi ambiri chikwanira; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Munthu woteroyo, pafupi nonse mwamtsutsa, choncho chilangocho nchokwanira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Chilango chimene ambiri a inu mwamupatsa munthu ameneyu nʼchokwanira. |
Chifukwa cha ichi ndilembera izi pokhala palibe ine, kuti pokhala ndili pomwepo ndingachite mowawitsa, monga mwa ulamuliro umene Ambuye anandipatsa ine wakumangirira, ndipo si wakugwetsa.
Pakuti, taonani, ichi chomwe, chakuti mudamvetsedwa chisoni cha kwa Mulungu, khama lalikulu lanji chidalichita mwa inu, komanso chodzikonza, komanso mkwiyo, komanso mantha, komanso kukhumbitsa komanso changu, komanso kubwezera chilango! M'zonse munadzitsimikizira nokha kuti muli oyera mtima m'menemo.