Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?
2 Akorinto 13:12 - Buku Lopatulika Mupatsane moni ndi kupsompsonana kopatulika. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mupatsane moni ndi chipsompsono chopatulika. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mupatsane moni mwa chikondi choona. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Lonjeranani ndi mpsopsono wachiyero. |
Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?
Mupatsane moni wina ndi mnzake ndi kupsompsonana kopatulika. Mipingo yonse ya Khristu ikupatsani moni.
Mupatsane moni ndi kupsompsonana kwa chikondi. Mtendere ukhale ndi inu nonse muli mwa Khristu.