Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Akorinto 16:20 - Buku Lopatulika

20 Akupatsani moni abale onse. Mupatsane moni ndi kupsompsonana kopatulika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Akupatsani moni abale onse. Mupatsane moni ndi kupsompsona kopatulika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Abale onse akuti moni. Mupatsane moni mwa chikondi chenicheni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Abale onse kuno akupereka moni wawo. Patsanani moni wachikondi chenicheni.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 16:20
10 Mawu Ofanana  

Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?


Mupatsane moni wina ndi mnzake ndi kupsompsonana kopatulika. Mipingo yonse ya Khristu ikupatsani moni.


Timoteo wantchito mnzanga akupatsani moni; ndi Lusio ndi Yasoni ndi Sosipatere, abale anga.


Gayo, mwini nyumba wolandira ine, ndi Mpingo wonse wa Ambuye, akupereka moni. Erasto, ndiye woyang'anira mzinda, akupereka moni, ndiponso Kwarto mbaleyo.


Oyera mtima onse akupatsani inu moni, koma makamaka iwo a banja la Kaisara.


Perekani moni kwa abale onse ndi chipsompsono chopatulika.


Perekani moni kwa atsogoleri anu onse, ndi oyera mtima onse. Akupatsani moni iwo a ku Italiya.


Mupatsane moni ndi kupsompsonana kwa chikondi. Mtendere ukhale ndi inu nonse muli mwa Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa