Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




1 Samueli 16:9 - Buku Lopatulika

Pamenepo Yese anapititsapo Sama. Ndipo anati, Koma uyunso Yehova sanamsankhe.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Pamenepo Yese anapititsapo Sama. Ndipo anati, Koma uyunso Yehova sanamsankhe.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Pamenepo Yese adaitana Sama kuti apite kwa Samuele. Koma Samuele adati, “Ameneyunso Chauta sadamsankhe.”

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Ndipo Yese anayitana Sama, koma Samueli anati, “Ngakhale uyu Yehova sanamusankhe.”

Onani mutuwo



1 Samueli 16:9
5 Mawu Ofanana  

Koma Aminoni anali ndi bwenzi lake, dzina lake ndiye Yonadabu, mwana wa Simea, mbale wa Davide. Ndipo Yonadabu anali munthu wochenjera ndithu.


Benabinadabu ku mtunda wa Dori, mkazi wake ndiye Tafati mwana wa Solomoni;


ndi Yese anabala mwana wake wamwamuna woyamba Eliyabu, ndi Abinadabu wachiwiri, ndi Simea wachitatu,


Ndipo Yese anapititsapo ana ake aamuna asanu ndi awiri. Koma Samuele anati kwa Yese, Yehova sanawasankhe awa.


Ndipo ana atatu aakulu a Yese anatsata Saulo kunkhondoko; ndi maina ao a ana ake atatuwo adapita ku nkhondowo ndiwo Eliyabu woyambayo, ndi mnzake womponda pamutu pake Abinadabu, ndi wachitatu Sama.