Pamenepo aiphe ng'ombeyo pamaso pa Yehova; ndipo ana a Aroni, ansembewo, abwere nao mwazi, nawaze mwaziwo pozungulira paguwa la nsembe, lokhala pa khoma la chihema chokomanako.
1 Samueli 1:25 - Buku Lopatulika Ndipo iwo anapha ng'ombe, nabwera naye mwanayo kwa Eli. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iwo anapha ng'ombe, nabwera naye mwanayo kwa Eli. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kumeneko adapha ng'ombe yamphongo ija ndipo mwanayo adampereka kwa Eli. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsono anapha ngʼombe yamphongo ija ndi kupereka mwana uja kwa Eli. |
Pamenepo aiphe ng'ombeyo pamaso pa Yehova; ndipo ana a Aroni, ansembewo, abwere nao mwazi, nawaze mwaziwo pozungulira paguwa la nsembe, lokhala pa khoma la chihema chokomanako.
Ndipo pamene anakwanira masiku a kukonza kwao, monga mwa chilamulo cha Mose, iwo anakwera naye kunka ku Yerusalemu, kukamsonyeza Iye kwa Ambuye,