1 Akorinto 8:2 - Buku Lopatulika Ngati wina ayesa kuti adziwa kanthu sanayambe kudziwa monga ayenera kudziwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ngati wina ayesa kuti adziwa kanthu sanayambe kudziwa monga ayenera kudziwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Munthu amene amadziyesa wodziŵa kanthu, ndiye kuti sakudziŵabe kwenikweni monga momwe akadayenera kudziŵira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Munthu amene amaganiza kuti amadziwa kanthu, ndiye kuti sakudziwa monga mmene amayenera kudziwira. |
Pakuti sindifuna, abale, kuti mukhale osadziwa chinsinsi ichi, kuti mungadziyese anzeru mwa inu nokha, kuti kuuma mtima kunadza pang'ono pa Israele, kufikira kudzaza kwa anthu amitundu kunalowa;
Pakuti tsopano tipenya m'kalirole, ngati chimbuuzi; koma pomwepo maso ndi maso. Tsopano ndizindikira mderamdera; koma pomwepo ndidzazindikiratu, monganso ndazindikiridwa.
Munthu asadzinyenge yekha; ngati wina ayesa kuti ali wanzeru mwa inu m'nthawi ino ya pansi pano, akhale wopusa, kuti akakhale wanzeru.