Numeri 2:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 74,600. Onani mutuwoBuku Lopatulika4 Ndipo khamu lake, ndi owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi asanu ndi awiri, mphambu zinai, kudza mazana asanu ndi limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo khamu lake, ndi owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi asanu ndi awiri, mphambu zinai, kudza mazana asanu ndi limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 ndipo ankhondo ake ngokwanira 74,600. Onani mutuwo |