Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Netanieli mwana wa Zuwara, kuchokera ku fuko la Isakara,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Wa Isakara, Netanele mwana wa Zuwara.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Wa Isakara, Netanele mwana wa Zuwara.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 fuko la Isakara, Netanele mwana wa Zuwara;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:8
5 Mawu Ofanana  

Naasoni mwana wa Aminadabu, kuchokera ku fuko la Yuda,


Eliabu mwana wa Heloni, kuchokera ku fuko la Zebuloni,


Mtsogoleri wa gulu la fuko la Isakara anali Netanieli mwana wa Zuwara,


Fuko la Isakara lidzamanga pafupi ndi Yuda. Mtsogoleri wa gulu la Isakara ndi Netanieli mwana wa Zuwara.


Pa tsiku lachiwiri, Natanieli mwana wa Zuwara, mtsogoleri wa Isakara, anabweretsa chopereka chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa