Eksodo 9:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma ngati ukana kuti apite ndi kupitiriza kuwaletsa, Onani mutuwoBuku Lopatulika2 Pakuti ukakana kuwalola amuke, ndi kuwagwira chigwiritsire, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti ukakana kuwalola amuke, ndi kuwagwira chigwiritsire, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma ukakananso kuŵalola kuti apite, ndi kuŵaletsa ndithu, Onani mutuwo |