Eksodo 1:16 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “Mukamathandiza amayi a Chihebri pa mwala wochirira, muzionetsetsa kuti akabadwa mwana wamwamuna muzipha, koma akakhala wamkazi muzimuleka akhale ndi moyo.” Onani mutuwoBuku Lopatulika16 ninati, Pamene muchiza akazi a Ahebri nimuwaone pamipando; akakhala mwana wamwamuna, mumuphe; akakhala wamkazi, akhale ndi moyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 ninati, Pamene muchiza akazi a Ahebri nimuwaone pamipando; akakhala mwana wamwamuna, mumuphe; akakhala wamkazi, akhale ndi moyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 “Mukamathandiza azimai achihebri pochira, akabadwa mwana wamwamuna, mupheni, akakhala wamkazi, mlekeni.” Onani mutuwo |