Danieli 5:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Choncho mfumu Belisazara anachita mantha koposa ndipo nkhope yake inapitirira kusinthika. Akalonga ake anathedwa nzeru. Onani mutuwoBuku Lopatulika9 Ndipo mfumu Belisazara anavutika kwambiri, ndi nkhope yake inasandulika, ndi akulu ake anathedwa nzeru. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo mfumu Belisazara anavutika kwambiri, ndi nkhope yake inasandulika, ndi akulu ake anathedwa nzeru. Onani mutuwo |