Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 2:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Davide anatenganso anthu amene anali nawo aliyense ndi banja lake, ndipo anakakhala ku midzi ya ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

3 Ndipo Davide anakwera nao anyamata ake okhala naye, munthu yense ndi banja lake; iwowa nakhala m'midzi ya Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo Davide anakwera nao anyamata ake okhala naye, munthu yense ndi banja lake; iwowa nakhala m'midzi ya Hebroni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Ndipo Davide adabwera ndi anthu ake aja amene anali nawo, aliyense ndi banja lake. Adakhala m'midzi ya ku Hebroni.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 2:3
7 Mawu Ofanana  

Nachi chiwerengero cha magulu a anthu ankhondo amene anabwera kwa Davide ku Hebroni kudzapereka ufumu wa Sauli kwa iye, monga momwe ananenera Yehova:


Ndipo aliyense amene anali pa mavuto, kapena ndi ngongole kapenanso amene anali wosakondwa anasonkhana kwa iye, ndipo iye anakhala mtsogoleri wawo. Onse pamodzi analipo amuna 400.


Pa tsiku lachitatu, Davide ndi anthu ake anakafika ku Zikilagi. Tsono anapeza Aamaleki atawononga kale dera la Negevi ndi Zikilagi. Anathira nkhondo mzinda wa Zikilagi ndi kuwutentha ndi moto.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa