2 Samueli 2:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Davide anakwera nao anyamata ake okhala naye, munthu yense ndi banja lake; iwowa nakhala m'midzi ya Hebroni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Davide anakwera nao anyamata ake okhala naye, munthu yense ndi banja lake; iwowa nakhala m'midzi ya Hebroni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndipo Davide adabwera ndi anthu ake aja amene anali nawo, aliyense ndi banja lake. Adakhala m'midzi ya ku Hebroni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Davide anatenganso anthu amene anali nawo aliyense ndi banja lake, ndipo anakakhala ku midzi ya ku Hebroni. Onani mutuwo |