Zekariya 7:3 - Buku Lopatulika3 nanene kwa ansembe a nyumba ya Yehova wa makamu, ndi kwa aneneri, ndi kuti, Kodi ndilire mwezi wachisanu, ndi kudzipatula, monga umo ndikachitira zaka izi zambiri? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 nanene kwa ansembe a nyumba ya Yehova wa makamu, ndi kwa aneneri, ndi kuti, Kodi ndilire mwezi wachisanu, ndi kudzipatula, monga umo ndikachitira zaka izi zambiri? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Kwinanso adaati akafunse ansembe a ku Nyumba ya Chauta Wamphamvuzonse ndiponso aneneri kuti, “Kodi ifeyo tizilira ndi kusala chakudya pa mwezi wachisanu monga m'mene takhala tikuchitira pa zaka zambiri?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 pokafunsa kwa ansembe a ku Nyumba ya Yehova Wamphamvuzonse ndi aneneri kuti, “Kodi ine ndizilira ndi kusala zakudya pa mwezi wachisanu, monga mmene ndakhala ndikuchitira pa zaka zambiri?” Onani mutuwo |