Zekariya 6:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo ndinayankha ndinati kwa mthenga wolankhula ndi ine, Izi nziyani, mbuyanga? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo ndinayankha ndinati kwa mthenga wolankhula ndi ine, Izi nziyani, mbuyanga? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono ndidafunsa mngelo amene ndinkalankhula naye uja kuti, “Mbuye wanga, kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndinafunsa mngelo amene amayankhula nane uja kuti, “Kodi mbuye wanga chimenechi nʼchiyani?” Onani mutuwo |