Zekariya 4:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo ndinayankha ndi kunena ndi mthenga wakulankhula ndi ine, ndi kuti, Izi nziyani mbuyanga? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo ndinayankha ndi kunena ndi mthenga wakulankhula ndi ine, ndi kuti, Izi nziyani mbuyanga? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndiye mngelo amene anali naneyo ndidamufunsa kuti “Mbuye wanga, kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndinamufunsa mngelo amene amayankhula nane kuti, “Kodi zimenezi nʼchiyani mbuye wanga?” Onani mutuwo |