Zekariya 2:7 - Buku Lopatulika7 Haya Ziyoni, thawa iwe wakukhala ndi mwana wamkazi wa Babiloni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Haya Ziyoni, thawa iwe wakukhala ndi mwana wamkazi wa Babiloni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tiyeni, thaŵirani ku Ziyoni, inu amene mudatengedwa ukapolo kupita ku Babiloni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 “Tuluka, iwe Ziyoni! Thawa, iwe amene umakhala mʼdziko la mwana wamkazi wa Babuloni!” Onani mutuwo |