Zekariya 11:2 - Buku Lopatulika2 Chema, mtengo wamlombwa, pakuti mkungudza wagwa, popeza mitengo yokoma yaipitsidwa; chemani athundu a ku Basani, pakuti nkhalango yotchinjirizika yagwa pansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Chema, mtengo wamlombwa, pakuti mkungudza wagwa, popeza mitengo yokoma yaipitsidwa; chemani athundu a ku Basani, pakuti nkhalango yotchinjirizika yagwa pansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Lirani mokweza, inu mitengo ya paini, pakuti mikungudza yagwa, mitengo yamphamvu yaonongeka. Lirani mokweza inu mitengo ya thundu ya ku Basani, pakuti nkhalango yoŵirira ija aiyeretsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Lira mwachisoni, iwe mtengo wa payini, pakuti mkungudza wagwa; mtengo wamphamvu wawonongeka! Lirani mwachisoni, inu mitengo ya thundu ya Basani; nkhalango yowirira yadulidwa! Onani mutuwo |