Zekariya 1:5 - Buku Lopatulika5 Makolo anu, ali kuti iwowo? Ndi aneneri, akhala ndi moyo kosatha kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Makolo anu, ali kuti iwowo? Ndi aneneri, akhala ndi moyo kosatha kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Kodi makolo anuwo ali kuti tsopano? Nanga aneneri, kodi amakhalapo mpaka muyaya? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Kodi makolo anuwo ali kuti tsopano? Nanga aneneri, kodi amakhalapo mpaka muyaya? Onani mutuwo |