Zefaniya 3:3 - Buku Lopatulika3 Akalonga ake m'kati mwake ndiwo mikango yobangula; oweruza ake ndi mimbulu ya madzulo, sasiya kanthu ka mawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Akalonga ake m'kati mwake ndiwo mikango yobangula; oweruza ake ndi mimbulu ya madzulo, sasiya kanthu ka mawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nduna zake zinkakhuluma m'kati mwake, ngati mikango yobangula. Oweruza ake anali ngati mimbulu yoyenda madzulo, yosasiyako ndi fupa lomwe kuti lifike mpaka m'maŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Akuluakulu ake ali ngati mikango yobuma, olamulira ake ndi olusa ngati mimbulu ya nthawi ya madzulo, zimene pofika mmawa sizisiya chilichonse. Onani mutuwo |