Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yuda 1:5 - Buku Lopatulika

5 Koma ndifuna kukukumbutsani mungakhale munadziwa zonse kale, kuti Ambuye, atapulumutsa mtundu wa anthu ndi kuwatulutsa m'dziko la Ejipito, anaononganso iwo osakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Koma ndifuna kukukumbutsani mungakhale munadziwa zonse kale, kuti Ambuye, atapulumutsa mtundu wa anthu ndi kuwatulutsa m'dziko la Ejipito, anaononganso iwo osakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Tsopano ndati ndikukumbutseni zina, ngakhale mudazidziŵa kale zonse. Paja Ambuye adaapulumutsa mtundu wa Aisraele ku dziko la Ejipito, koma pambuyo pake adaŵaononga onse amene sadakhulupirire.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ngakhale munazidziwa kale zonsezi, ndafuna kuti ndikukumbutseni kuti Ambuye anapulumutsa anthu ake ndi kuwatulutsa mʼdziko la Igupto, koma pambuyo pake anawononga amene sanakhulupirire.

Onani mutuwo Koperani




Yuda 1:5
14 Mawu Ofanana  

Potero anawasamulira dzanja lake, kuti awagwetse m'chipululu:


Ndipo kunakhala tsiku lomwelo, kuti Yehova anatulutsa ana a Israele m'dziko la Ejipito, monga mwa makamu ao.


Koma mwina ndaposa kukulemberani molimba mtima monga kukukumbutsaninso, chifukwa cha chisomo chapatsidwa kwa ine ndi Mulungu,


Koma m'chinthu ichi simunakhulupirire Yehova Mulungu wanu,


Pakuti ndi ayani, pakumva, anapsetsa mtima? Kodi si onse aja adatuluka mu Ejipito ndi Mose?


Okondedwa, iyi ndiye kalata yachiwiri ndilembera kwa inu tsopano; mwa onse awiri nditsitsimutsa mtima wanu woona ndi kukukumbutsani;


Ndipo inu muli nako kudzoza kochokera kwa Woyerayo, ndipo mudziwa zonse.


Sindinakulembereni chifukwa simudziwa choonadi, koma chifukwa muchidziwa, ndi chifukwa kulibe bodza lochokera kwa choonadi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa