Yoweli 3:9 - Buku Lopatulika9 Mulalikire ichi mwa amitundu, mukonzeretu nkhondo; utsani amuna amphamvu; amuna onse a nkhondo ayandikire nakwere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mulalikire ichi mwa amitundu, mukonzeretu nkhondo; utsani amuna amphamvu; amuna onse a nkhondo ayandikire nakwere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Mulengeze pakati pa anthu a mitundu ina kuti, ‘Konzekerani nkhondo, itanani ankhondo amphamvu. Asilikali onse afike pafupi, ayambe nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Lengezani izi pakati pa anthu a mitundu ina: Konzekerani nkhondo! Dzutsani ankhondo amphamvu! Asilikali onse afike pafupi ndipo ayambe nkhondo. Onani mutuwo |