Yoweli 3:7 - Buku Lopatulika7 taonani, ndidzawautsa kumalo kumene munawagulitsako, ndi kubwezera chilango chanu pamutu panu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 taonani, ndidzawautsa kumalo kumene munawagulitsako, ndi kubwezera chilango chanu pamutu panu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma ndidzaŵadzutsa kuti achoke kumalo kumene mudaŵagulitsa. Kenaka ndidzabwezera zochita zanu zonse pamutu panu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 “Taonani, Ine ndidzawachotsa kumalo kumene munawagulitsako, ndipo ndidzabwezera zimene mwachita pa mitu yanu. Onani mutuwo |