Yoweli 3:6 - Buku Lopatulika6 munagulitsanso ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu kwa ana a Yavani, kuwachotsa kutali kwa malire ao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 munagulitsanso ana a Yuda ndi ana a Yerusalemu kwa ana a Yavani, kuwachotsa kutali kwa malire ao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mudakagulitsa anthu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu kwa Agriki, kuti mupite nawo kutali ndi malire a dziko lao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Inu munagulitsa anthu a ku Yuda ndi Yerusalemu kwa Agriki, kuti apite kutali ndi malire a dziko lawo. Onani mutuwo |