Yoweli 2:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo ndidzaonetsa zodabwitsa kuthambo ndi padziko lapansi, mwazi, ndi moto, ndi utsi tolo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo ndidzaonetsa zodabwitsa kuthambo ndi pa dziko lapansi, mwazi, ndi moto, ndi utsi tolo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 “Mu mlengalenga ndi pa dziko lapansi ndidzaonetsa zodabwitsa izi: magazi, moto ndi utsi watoloo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndidzaonetsa zodabwitsa mlengalenga ndi pa dziko lapansi, ndizo magazi, moto ndi utsi watolotolo. Onani mutuwo |