Yoweli 2:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo madwale adzakhala ndi tirigu, ndi vinyo, ndi mafuta; zidzasefuka m'zosungiramo zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo madwale adzakhala ndi tirigu, ndi vinyo, ndi mafuta; zidzasefuka m'zosungiramo zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 “Pa malo opunthira padzadzaza tirigu. Mopondera mphesa mudzasefukira vinyo watsopano, mafutanso adzachuluka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pa malo opunthira padzaza tirigu; mʼmitsuko mudzasefukira vinyo watsopano ndi mafuta. Onani mutuwo |